1 Akorinto 15:13 - Buku Lopatulika13 Koma ngati kulibe kuuka kwa akufa, Khristunso sanaukitsidwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma ngati kulibe kuuka kwa akufa, Khristunso sanaukitsidwa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ngati akufa sadzauka, ndiye kuti Khristunso sadauke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ngati kulibe kuuka kwa akufa, ndiye kuti ngakhale Khristu sanaukenso. Onani mutuwo |