Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Akorinto 14:30 - Buku Lopatulika

30 Koma ngati kanthu kuvumbulutsidwa kwa wina wakukhalapo, akhale chete woyambayo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Koma ngati kanthu kuvumbulutsidwa kwa wina wakukhalapo, akhale chete woyambayo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Koma Mulungu akaulula kanthu kwa munthu wina amene ali pomwepo, amene akulankhulayo akhale chete.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Ndipo ngati vumbulutso labwera kwa munthu amene wakhala pansi, amene akuyankhulayo akhale chete.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 14:30
8 Mawu Ofanana  

Taonani, ndinalindira mau anu, ndinatcherera khutu zifukwa zanu, pofunafuna inu ponena.


Nanga chiyani tsono, abale? Pamene musonkhana, yense ali nalo salimo, ali nacho chiphunzitso, ali nalo vumbulutso, ali nalo lilime, ali nacho chimasuliro. Muchite zonse kukumangirira.


Ndipo aneneri alankhule awiri kapena atatu, ndi ena azindikire.


Pakuti mukhoza nonse kunenera mmodzimmodzi, kuti onse aphunzire, ndi onse afulumidwe;


Koma tsopano, abale, ngati ndidza kwa inu ndi kulankhula malilime, ndikakupindulitsani chiyani, ngati sindilankhula ndi inu kapena m'vumbulutso, kapena m'chidziwitso, kapena m'chinenero, kapena m'chiphunzitso?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa