1 Akorinto 14:18 - Buku Lopatulika18 Ndiyamika Mulungu kuti ndilankhula malilime koposa inu nonse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndiyamika Mulungu kuti ndilankhula malilime koposa inu nonse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndikuthokoza Mulungu kuti ine ndimalankhula m'zilankhulo zosadziŵika kuposa nonsenu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndikuyamika Mulungu chifukwa ndimayankhula malilime kuposa nonsenu. Onani mutuwo |