1 Akorinto 14:14 - Buku Lopatulika14 Pakuti ngati ndipemphera m'lilime, mzimu wanga upemphera, koma chidziwitso changa chikhala chosabala kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pakuti ngati ndipemphera m'lilime, mzimu wanga upemphera, koma chidziwitso changa chikhala chosabala kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ngati ndipemphera m'chilankhulo chosadziŵika, mtima wanga ukupemphera inde, koma nzeru zanga sizipindulapo kanthu pamenepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Popeza ngati ndipemphera mʼmalilime, ndi mzimu wanga umene ukupemphera, koma nzeru zanga sizikupindula kanthu. Onani mutuwo |