1 Akorinto 14:12 - Buku Lopatulika12 Momwemo inunso, popeza muli ofunitsitsa mphatso za Mzimu, funani kuti mukachuluke kukumangirira kwa Mpingo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Momwemo inunso, popeza muli ofunitsitsa mphatso za Mzimu, funani kuti mukachuluke kukumangirira kwa Mpingo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Inunso chimodzimodzi: popeza kuti mwaika mtima pa mphatso za Mzimu Woyera, muziyesetsa kuzigwiritsa ntchito, makamaka mphatso zolimbikitsa mpingo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Chimodzimodzinso inu. Popeza mumafunitsitsa mphatso za Mzimu, yesetseni kuchita bwino pa mphatso zimene zimamanga mpingo. Onani mutuwo |