Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Akorinto 12:30 - Buku Lopatulika

30 Ali nazo mphatso za machiritso onse kodi? Kodi onse alankhula ndi malilime? Kodi onse amasulira mau?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ali nazo mphatso za machiritso onse kodi? Kodi onse alankhula ndi malilime? Kodi onse amasulira mau?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Kodi onse ali ndi mphatso ya kuchiritsa matenda? Kodi onse angathe kulankhula zilankhulo zosadziŵika? Kodi onse angathe kuzitanthauzira?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Kodi onse ali ndi mphatso zamachiritso? Kodi onse amayankhula malilime? Kodi onse amatanthauzira malilime?

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 12:30
5 Mawu Ofanana  

ndi kwa wina machitidwe a mphamvu; ndi kwa wina chinenero; ndi kwa wina chizindikiro cha mizimu; kwa wina malilime a mitundumitundu; ndi kwa wina mamasulidwe a malilime.


Ndipotu Mulungu anaika ena mu Mpingo, poyamba atumwi, achiwiri aneneri, achitatu aphunzitsi, pamenepo zozizwa, pomwepo mphatso za machiritso, mathandizo, maweruziro, malilime a mitundumitundu.


Kodi ali onse atumwi? Ali aneneri onse kodi? Ali aphunzitsi onse? Ali onse ochita zozizwa?


kwa wina chikhulupiriro, mwa Mzimu yemweyo; ndi kwa wina mphatso za machiritso, mwa Mzimu mmodziyo;


Chifukwa chake wolankhula lilime, apemphere kuti amasule.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa