1 Akorinto 12:29 - Buku Lopatulika29 Kodi ali onse atumwi? Ali aneneri onse kodi? Ali aphunzitsi onse? Ali onse ochita zozizwa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Kodi ali onse atumwi? Ali aneneri onse kodi? Ali aphunzitsi onse? Ali onse ochita zozizwa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Kodi onse ndi atumwi? Kodi onse ndi aneneri? Kodi onse ndi aphunzitsi? Kodi onse ali ndi mphamvu za kuchita zozizwitsa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Kodi onse ndi atumwi? Kodi onse ndi aneneri? Kodi onse ndi aphunzitsi? Kodi onse amachita zozizwitsa? Onani mutuwo |