Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Akorinto 12:25 - Buku Lopatulika

25 kuti kusakhale chisiyano m'thupi; koma kuti ziwalo zifanane ndi kusamalana china ndi chinzake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 kuti kusakhale chisiyano m'thupi; koma kuti ziwalo zifanane ndi kusamalana china ndi chinzake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Adachita zimenezi kuti pasakhale kugaŵikana m'thupi, koma kuti ziwalo zonse zizisamalirana.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 kuti pasakhale kugawikana mʼthupi koma kuti ziwalo zonse zisamalirane.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 12:25
8 Mawu Ofanana  

Koma zokoma zathu zilibe kusowa; koma Mulungu analumikizitsa thupi, napatsa ulemu wochuluka kwa chosowacho;


Ndipo chingakhale chiwalo chimodzi chimva chowawa, ziwalo zonse zimva pamodzi; chingakhale chimodzi chilemekezedwa, ziwalo zonse zikondwera nacho pamodzi.


pakuti, pokhala pali nkhwidzi ndi ndeu pakati pa inu simuli athupi kodi, ndi kuyendayenda monga mwa munthu?


Chotsalira, abale, kondwerani. Muchitidwe angwiro; mutonthozedwe; khalani a mtima umodzi, khalani mumtendere; ndipo Mulungu wa chikondi ndi mtendere akhale pamodzi ndi inu.


Chifukwa chake ndingakhale ndalembera kwa inu, sindinachita chifukwa cha iye amene anachita choipa, kapena chifukwa cha iye amene anachitidwa choipa, koma kuti khama lanu la kwa ife lionetsedwe kwa inu pamaso pa Mulungu.


Koma ayamikike Mulungu, wakupatsa khama lomweli la kwa inu mu mtima wa Tito.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa