1 Akorinto 12:24 - Buku Lopatulika24 Koma zokoma zathu zilibe kusowa; koma Mulungu analumikizitsa thupi, napatsa ulemu wochuluka kwa chosowacho; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Koma zokoma zathu zilibe kusowa; koma Mulungu analumikizitsa thupi, napatsa ulemu wochuluka kwa chosowacho; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Koma zimene zili zooneka bwino, nkosafunikira kuti tiziveke motero. Mulungu polumikiza ziwalo za thupi, adazilumikiza mwa njira yoti adapereka ulemu woposa kwa ziwalo zimene zimausoŵadi ulemuwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Koma ziwalo zooneka bwino, nʼkosafunika kuti tizisamalire mwapadera. Mulungu polumikiza ziwalo zathupi, anapereka ulemu wopambana kwa ziwalo zimene zimafunadi ulemuwo Onani mutuwo |