1 Akorinto 12:20 - Buku Lopatulika20 Koma tsopano pali ziwalo zambiri, koma thupi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma tsopano pali ziwalo zambiri, koma thupi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Komatu ziwalo nzambiri, ngakhale thupi ndi limodzi lokha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Mmene zililimu, pali ziwalo zambiri koma thupi ndi limodzi lokha. Onani mutuwo |