1 Akorinto 12:19 - Buku Lopatulika19 Koma ngati zonse zikadakhala chiwalo chimodzi, likadakhala kuti thupi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Koma ngati zonse zikadakhala chiwalo chimodzi, likadakhala kuti thupi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ziwalo zonse zikadangokhala chiwalo chimodzi, sipakadakhala thupi konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Nanga zonse zikanakhala chiwalo chimodzi, ndiye thupi likanakhala lotani? Onani mutuwo |