1 Akorinto 12:14 - Buku Lopatulika14 Pakutinso thupi silikhala chiwalo chimodzi, koma zambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pakutinso thupi silikhala chiwalo chimodzi, koma zambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Thupitu si chiwalo chimodzi chokha ai, koma lili ndi ziwalo zambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Tsopano thupi silinapangidwe ndi chiwalo chimodzi koma ndi ziwalo zambiri. Onani mutuwo |