1 Akorinto 11:31 - Buku Lopatulika31 Koma ngati tikadadzizindikira tokha sitikadaweruzidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Koma ngati tikadadzizindikira tokha sitikadaweruzidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Tikadadziyang'ana bwino, sitikadalangidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Koma tikanadziyesa tokha sitikaweruzidwanso. Onani mutuwo |