1 Akorinto 11:29 - Buku Lopatulika29 Pakuti iye wakudya ndi wakumwa, adya namwa chiweruziro kwa iye yekha, ngati sazindikira thupilo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Pakuti iye wakudya ndi wakumwa, adya namwa chiweruziro kwa iye yekha, ngati sazindikira thupilo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Pakuti amene adya mkate umenewu ndi kumwa chikho chimenechi, koma osalizindikira thupi la Ambuye, akudziitanira chilango pamene akudya ndi kumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Popeza aliyense amene adya kapena kumwa mosazindikira thupi la Ambuye, amadya ndi kumwa chiweruzo chake chomwe. Onani mutuwo |