1 Akorinto 11:19 - Buku Lopatulika19 Pakuti kuyenera kuti pakhale mipatuko mwa inu, kuti iwo ovomerezedwa aonetsedwe mwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Pakuti kuyenera kuti pakhale mipatuko mwa inu, kuti iwo ovomerezedwa aonetsedwe mwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Nkofunika ndithu kuti pakhale kusiyana maganizo pakati panu, kuti amene ali okhoza pakati panu adziŵike. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Nʼzosakayikitsa kuti pali kugawikana pakati panu kuti adziwike amene ndi ovomerezeka ndi Mulungu. Onani mutuwo |