Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




1 Akorinto 11:14 - Buku Lopatulika

14 Kodi ubadwidwe womwe sutiphunzitsa kuti ngati mwamuna aweta tsitsi chinyozetsa iye?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Kodi ubadwidwe womwe sutiphunzitsa kuti ngati mwamuna aweta tsitsi chinyozetsa iye?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Kodi chibadwa chathu chomwe sichitiphunzitsa kuti nchamanyazi kwa mwamuna kukhala ndi tsitsi lalitali,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Kodi chikhalidwe chathu sichitiphunzitsa kuti nʼchamanyazi kuti mwamuna akhale ndi tsitsi lalitali,

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 11:14
5 Mawu Ofanana  

Ndipo pometa tsitsi lake amameta potsiriza chaka, chifukwa tsitsi linamlemerera, chifukwa chake atalimeta anayesa tsitsi la pamutu wake, napeza masekeli mazana awiri, monga mwa muyeso wa mfumu.


Yesu anayankha, Ndilibe chiwanda Ine; koma ndilemekeza Atate wanga, ndipo inu mundipeputsa.


Lingirirani mwa inu nokha: Kodi nkuyenera kuti apemphere kwa Mulungu, wosafunda mutu?


Koma ngati mkazi aweta tsitsi, kuli ulemerero kwa iye; pakuti tsitsi lake lapatsidwa kwa iye ngati chophimba.


Koma ngati afuna kuphunzira kanthu afunse amuna ao a iwo okha kwao; pakuti kunyazitsa mkazi kulankhula mu Mpingo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa