1 Akorinto 10:27 - Buku Lopatulika27 Ngati wina wa osakhulupirira akuitanani, ndipo mufuna kupita; mudye chomwe chiikidwa kwa inu, osafunsa kanthu, chifukwa cha chikumbumtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ngati wina wa osakhulupirira akuitanani, ndipo mufuna kupita; mudye chomwe chiikidwa kwa inu, osafunsa kanthu, chifukwa cha chikumbu mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Mkunja akakuitanani kuti mukadye naye, inuyo nkuvomera kupitako, mukadye chilichonse chimene akakupatseni. Musakafunse mafunso okhudzana ndi m'mene mtima wanu umamvera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Ngati wosakhulupirira akuyitanani kuti mukadye naye, inuyo ndi kuvomera kupitako, mukadye chilichonse chimene akakupatseni ndipo musakafunse mafunso okhudzana ndi chikumbumtima chanu. Onani mutuwo |