1 Akorinto 10:24 - Buku Lopatulika24 Munthu asafune zake za iye yekha, koma za mnzake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Munthu asafune zake za iye yekha, koma za mnzake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Munthu asamangodzifunira yekha zabwino, koma makamaka azifunira anzake zabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Munthu aliyense asafunefune zokomera iye yekha, koma zokomeranso ena. Onani mutuwo |