1 Akorinto 10:19 - Buku Lopatulika19 Ndinena chiyani tsono? Kuti choperekedwa nsembe kwa mafano chili kanthu? Kapena kuti fano lili kanthu kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndinena chiyani tsono? Kuti choperekedwa nsembe kwa mafano chili kanthu? Kapena kuti fano lili kanthu kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono tanthauzo la zimene ndikunenazi nchiyani? Kodi ndiye kuti nsembe yoperekedwa kwa fano nkanthu? Kapena kuti fanolo nkanthu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Kodi ndikutanthauza kuti nsembe zoperekedwa kwa mafano ndi kanthu konse, kapena kuti mafano ndi kanthu konse? Onani mutuwo |