1 Akorinto 10:15 - Buku Lopatulika15 Ndinena monga kwa anzeru; lingirirani inu chimene ndinena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndinena monga kwa anzeru; lingirirani inu chimene ndinena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ndikulankhula nanu ngati anthu anzeru. Muweruze nokha zimene ndikunenazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndikuyankhula kwa a anthu anzeru zawo, nokha muweruze pa zimene ndikunenazi. Onani mutuwo |