Nahumu INTRO1 - Buku LopatulikaMau Oyamba Bukuli ndi ndakatulo yokondwerera kupasuka kwa Ninive, mzinda waukulu wa Aasiriya amene ankazunza Aisraele kuyambira kale. Kupasuka kwa mzindawo kuwoneka ngati chilango cha Mulungu chogwera anthu onyada ndi ankhanza. Za mkatimu Chauta aimba Ninive mlandu 1.1-15 Kupasuka kwa mzindawo 2.1—3.19 |
Bible Society of Malawi
Bible Society of Malawi