3 Yohane INTRO1 - Buku LopatulikaMau Oyamba Kalata yachitatu yolembedwa ndi mtumwi Yohane inalembedwa ndi “Mkuluyo” kulembera mtsogoleri wa mpingo dzina lake Gayo. Mlembiyo akumuyamikira Gayo chifukwa cha kuthandiza Akhristu ena, komanso akuwachenjeza za munthu wina dzina lake Diotrefe. Za mkatimu Mau oyamba 1.1-4 Gayo akumulemekeza 1.5-8 Diotrefe akumudzudzula 9-10 Demetrio akumuyamikira 1.11-12 Mau omaliza 1.13-15 |
Bible Society of Malawi
Bible Society of Malawi