Numeri 26:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Utatha mliri Yehova anati kwa Mose ndi Eliezara mwana wa Aaroni, Buku Lopatulika Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Utatha mliriwo, Chauta adauza Mose ndi Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti, |
chifukwa ankakuonani inu ngati adani awo pamene anakupusitsani pa nkhani ya ku Peori, ndiponso za mlongo wawo Kozibi, mwana wamkazi wa mtsogoleri wa Amidiyani, mkazi yemwe anaphedwa pamene mliri unabwera chifukwa cha zimene zinachitika ku Peori.”