Numeri 2:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 74,600. Buku Lopatulika Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri, mphambu zinai, kudza mazana asanu ndi limodzi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi asanu ndi awiri, mphambu zinai, kudza mazana asanu ndi limodzi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndipo ankhondo ake ngokwanira 74,600. |
Kummawa, kotulukira dzuwa, magulu a msasa wa Yuda amange pamene pali mbendera yawo. Mtsogoleri wa Ayudawo ndi Naasoni mwana wa Aminadabu.
Fuko la Isakara lidzamanga pafupi ndi Yuda. Mtsogoleri wa gulu la Isakara ndi Netanieli mwana wa Zuwara.