Yehova atawamva anakwiya kwambiri; moto wake unayaka kutsutsana ndi Yakobo, ndipo mkwiyo wake unauka kutsutsana ndi Israeli,
Numeri 11:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Motero malowo anawatcha Tabera, chifukwa moto wa Yehova unayaka pakati pawo. Buku Lopatulika Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anatcha malowo dzina lake Tabera; popeza moto wa Yehova udayaka pakati pao. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero malowo adaŵatcha Tabera, chifukwa choti moto wa Chauta udayaka pakati pao. |
Yehova atawamva anakwiya kwambiri; moto wake unayaka kutsutsana ndi Yakobo, ndipo mkwiyo wake unauka kutsutsana ndi Israeli,
Anthu ena osokoneza amene anali pakati pa Aisraeli anayamba kukhumba chakudya cha ku Igupto ndipo Aisraeli nawonso anayamba kufuwula kwambiri nʼkumati, “Tikanangopeza nyama yoti nʼkudya!
Ndipo moto wochokera kwa Yehova unabwera nʼkunyeketsa anthu 250 amene ankapereka nsembe yofukiza aja.