Mwa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efereimu, Elisama mwana wa Amihudi; kuchokera ku fuko la Manase, Gamalieli mwana wa Pedazuri;
Numeri 1:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Eliabu mwana wa Heloni, kuchokera ku fuko la Zebuloni, Buku Lopatulika Wa Zebuloni, Eliyabu mwana wa Heloni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa Zebuloni, Eliyabu mwana wa Heloni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa fuko la Zebuloni, Eliyabu mwana wa Heloni. |
Mwa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efereimu, Elisama mwana wa Amihudi; kuchokera ku fuko la Manase, Gamalieli mwana wa Pedazuri;
Lotsatira lidzakhala fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa gulu la Zebuloni ndi Eliabu mwana wa Heloni.
Pa tsiku lachitatu, Eliabu mwana wa Heloni, mtsogoleri wa Azebuloni, anabweretsa chopereka chake.