Numeri 1:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Netanieli mwana wa Zuwara, kuchokera ku fuko la Isakara, Buku Lopatulika Wa Isakara, Netanele mwana wa Zuwara. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa Isakara, Netanele mwana wa Zuwara. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa fuko la Isakara, Netanele mwana wa Zuwara; |
Fuko la Isakara lidzamanga pafupi ndi Yuda. Mtsogoleri wa gulu la Isakara ndi Netanieli mwana wa Zuwara.
Pa tsiku lachiwiri, Natanieli mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa Isakara, anabweretsa chopereka chake.