Aaroni anakwatira Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wa Nasoni ndipo Iye anabereka Nadabu, Abihu, Eliezara ndi Itamara.
Numeri 1:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Naasoni mwana wa Aminadabu, kuchokera ku fuko la Yuda, Buku Lopatulika Wa Yuda, Nasoni mwana wa Aminadabu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa Yuda, Nasoni mwana wa Aminadabu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa fuko la Yuda, Nasoni mwana wa Aminadabu; |
Aaroni anakwatira Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wa Nasoni ndipo Iye anabereka Nadabu, Abihu, Eliezara ndi Itamara.
Magulu a msasa wa Yuda ndiwo anayamba kunyamuka potsata mbendera yawo. Mtsogoleri wa gulu lawo anali Naasoni mwana wa Aminadabu.
Kummawa, kotulukira dzuwa, magulu a msasa wa Yuda amange pamene pali mbendera yawo. Mtsogoleri wa Ayudawo ndi Naasoni mwana wa Aminadabu.
Amene anabweretsa chopereka chake tsiku loyamba anali Naasoni mwana wa Aminadabu wa fuko la Yuda.