Mayina a anthu amene akuthandizeniwo ndi awa: Elizuri mwana wa Sedeuri, kuchokera ku fuko la Rubeni,
Numeri 1:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Selumieli mwana wa Zurisadai, kuchokera ku fuko la Simeoni, Buku Lopatulika Wa Simeoni, Selumiele mwana wa Zurishadai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa Simeoni, Selumiele mwana wa Zurishadai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa fuko la Simeoni, Selumiele mwana wa Zurishadai; |
Mayina a anthu amene akuthandizeniwo ndi awa: Elizuri mwana wa Sedeuri, kuchokera ku fuko la Rubeni,
Fuko la Simeoni lidzamanga pafupi ndi Rubeni. Mtsogoleri wa gulu la Simeoni ndi Selumieli mwana wa Zurisadai.
Pa tsiku lachisanu Selumieli mwana wa Zurisadai, mtsogoleri wa fuko la Simeoni, anabweretsa chopereka chake.