Adzakulangani ndi mivi yakuthwa ya munthu wankhondo, ndi makala oyaka a mtengo wa tsanya.
Masalimo 127:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana a pa unyamata ali ngati mivi mʼmanja mwa munthu wankhondo. Buku Lopatulika Ana a ubwana wake wa munthu akunga mivi m'dzanja lake la chiphona. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana a ubwana wake wa munthu akunga mivi m'dzanja lake la chiphona. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana apaunyamata ali ngati mivi m'manja mwa munthu wankhondo. |
Adzakulangani ndi mivi yakuthwa ya munthu wankhondo, ndi makala oyaka a mtengo wa tsanya.
Ana ake amamunyadira ndipo amamutcha kuti wodala; ndipo mwamuna wake, amamuyamikira nʼkumati,
Taonani, ndidzaukitsa gulu lankhondo lamphamvu la mitundu ina ndi kubwera nalo kuchokera kumpoto kudzamenyana ndi Babuloni. Iwo adzandandalika ankhondo awo ndi kugonjetsa Babuloni. Mivi yawo ili ngati ya ankhondo aluso, yosapita padera.