Eksodo 7:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anati kwa Mose ndi Aaroni, Buku Lopatulika Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Chauta adauza Mose ndi Aroni kuti, |
“Ngati Farao adzati kwa inu, ‘Chitani chozizwitsa,’ iwe Mose udzati kwa Aaroni, ‘Tenga ndodo yako ndipo uyiponye pamaso pa Farao,’ ndipo idzasanduka njoka.”
zizindikiro zozizwitsa zimene anazionetsa ndi zinthu zimene anazichita mʼkati mwa Igupto, Farao mfumu ya Igupto ndi kwa dziko lake lonse;