Eksodo 13:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anati kwa Mose, Buku Lopatulika Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adauzanso Mose kuti, |
muzikapereka kwa Ambuye ana onse oyamba kubadwa. Ziweto zonse zazimuna zoyamba kubadwa ndi za Ambuye.
“Ana onse aamuna oyamba kubadwa uwapatule, ndi anga. Aliyense woyamba kubadwa pakati pa Aisraeli ndi wanga, kaya ndi wa munthu kapena wa chiweto.”