Israeli akanali mʼderali, Rubeni anapita nakagonana ndi Biliha, mdzakazi wa abambo ake. Yakobo uja anazimva zimenezi. Yakobo anali ndi ana aamuna khumi ndi awiri:
Eksodo 1:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Dani, Nafutali; Gadi ndi Aseri. Buku Lopatulika Dani ndi Nafutali, Gadi ndi Asere. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Dani ndi Nafutali, Gadi ndi Asere. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Dani, Nafutali, Gadi ndi Asere. |
Israeli akanali mʼderali, Rubeni anapita nakagonana ndi Biliha, mdzakazi wa abambo ake. Yakobo uja anazimva zimenezi. Yakobo anali ndi ana aamuna khumi ndi awiri:
Amenewa ndi zidzukulu za Yakobo mwa Zilipa amene Labani anapereka kwa mwana wake, Leya. Onse pamodzi analipo 16.