Ana a Leya ndi awa: Rubeni anali mwana woyamba wa Yakobo, Simeoni, Levi, Yuda, Isakara, ndi Zebuloni.
Eksodo 1:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Isakara, Zebuloni, Benjamini; Buku Lopatulika Isakara, Zebuloni, ndi Benjamini; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Isakara, Zebuloni, ndi Benjamini; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Isakara, Zebuloni, Benjamini, |
Ana a Leya ndi awa: Rubeni anali mwana woyamba wa Yakobo, Simeoni, Levi, Yuda, Isakara, ndi Zebuloni.
Mzere wachinayi pakhale miyala ya topazi, onikisi ndi yasipa. Miyalayi uyiike mu zoyikamo zagolide.