Zekariya 8:1 - Buku Lopatulika Ndipo mau a Yehova wa makamu anadza kwa ine, ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mau a Yehova wa makamu anadza kwa ine, ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta Wamphamvuzonse adandipatsanso uthenga uwu wakuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Awa ndi mawu amene Yehova Wamphamvuzonse ananena. |
koma ndidzawabalalitsa ndi kamvulumvulu mwa amitundu onse amene sanawadziwe. Motero dziko linakhala bwinja, m'mbuyo mwao; palibe munthu wopitapo ndi kubwererako; pakuti adaika dziko lofunikalo labwinja.
Atero Yehova wa makamu: Ndimchitira nsanje Ziyoni ndi nsanje yaikulu, ndipo ndimchitira nsanje ndi ukali waukulu.