sitinamvere atumiki anu aneneri, amene ananena m'dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m'dziko.
Zekariya 7:8 - Buku Lopatulika Ndipo mau a Yehova anadza kwa Zekariya, ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mau a Yehova anadza kwa Zekariya, ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adapatsa Zekariya uthenga uwu wakuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo Yehova anayankhulanso ndi Zekariya kuti, |
sitinamvere atumiki anu aneneri, amene ananena m'dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m'dziko.
Si ndiwo mau Yehova anawalalikira mwa aneneri oyamba aja, muja Yerusalemu anali nao okhalamo, ndi wokhazikika; ndi m'mizinda mwake pozungulira pake, ndi m'dziko la kumwera, ndi m'chidikha munali anthu okhalamo?
Watero Yehova wa makamu, kuti, Weruzani chiweruzo choona, nimuchitire yense mnzake chifundo ndi ukoma mtima;