Chifukwa chake Ambuye, Yehova wa makamu, adzatumiza kuonda mwa onenepa ake; ndipo pansi pa ulemerero wake padzayaka kutentha, konga ngati kutentha kwa moto.
Zekariya 7:4 - Buku Lopatulika Ndipo mau a Yehova wa makamu anadza kwa ine, ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mau a Yehova wa makamu anadza kwa ine, ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Chauta Wamphamvuzonse adandipatsa uthenga uwu wakuti: Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo Yehova Wamphamvuzonse anayankhula nane kuti, |
Chifukwa chake Ambuye, Yehova wa makamu, adzatumiza kuonda mwa onenepa ake; ndipo pansi pa ulemerero wake padzayaka kutentha, konga ngati kutentha kwa moto.
nanene kwa ansembe a nyumba ya Yehova wa makamu, ndi kwa aneneri, ndi kuti, Kodi ndilire mwezi wachisanu, ndi kudzipatula, monga umo ndikachitira zaka izi zambiri?
Nena kwa anthu onse a m'dziko, ndi kwa ansembe, kuti, Muja mukasala ndi kulira mwezi wachisanu, ndi wachisanu ndi chitatu, zaka izi makumi asanu ndi awiri, kodi mukasalira Ine, Inedi?