Mwezi wachisanu ndi chitatu, chaka chachiwiri cha Dariusi, mau a Yehova anadza kwa Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido mneneri, ndi kuti,
Zekariya 6:9 - Buku Lopatulika Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, ndi kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, ndi kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kenaka Chauta adandipatsa uthenga wakuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anayankhula nane kuti, |
Mwezi wachisanu ndi chitatu, chaka chachiwiri cha Dariusi, mau a Yehova anadza kwa Zekariya mwana wa Berekiya, mwana wa Ido mneneri, ndi kuti,
Ndipo kunachitika chaka chachinai cha mfumu Dariusi, mau a Yehova anadza kwa Zekariya tsiku lachinai la mwezi wachisanu ndi chinai, ndiwo Kisilevi.