Ndinaona usiku, taonani, munthu woyenda pa kavalo wofiira, alikuima pakati pa mitengo yamchisu inali kunsi; ndi pambuyo pake panali akavalo ofiira, odera ndi oyera.
Zekariya 6:2 - Buku Lopatulika Ku galeta woyamba kunali akavalo ofiira; ndi kugaleta wachiwiri akavalo akuda; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ku galeta woyamba kunali akavalo ofiira; ndi kugaleta wachiwiri akavalo akuda; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Galeta loyamba linkakokedwa ndi akavalo ofiira, lachiŵiri akavalo akuda, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Galeta loyamba limakokedwa ndi akavalo ofiira, lachiwiri ndi akavalo akuda, |
Ndinaona usiku, taonani, munthu woyenda pa kavalo wofiira, alikuima pakati pa mitengo yamchisu inali kunsi; ndi pambuyo pake panali akavalo ofiira, odera ndi oyera.
Galeta wa akavalo akuda atulukira kudziko la kumpoto; ndi oyerawo atulukira kuwatsata; ndi amawanga atulukira kudziko la kumwera.
Ndipo chinaoneka chizindikiro china m'mwamba taonani, chinjoka chofiira, chachikulu, chakukhala nayo mitu isanu ndi iwiri, ndi nyanga khumi, ndi pamutu pake nduwira zachifumu zisanu ndi ziwiri.
Ndipo ananditenga kunka nane kuchipululu, mu Mzimu; ndipo ndinaona mkazi alinkukhala pachilombo chofiira, chodzala ndi maina a mwano, chakukhala nayo mitu isanu ndi iwiri ndi nyanga khumi.