Ukani Yehova, Mumtsekereze, mumgwetse, landitsani moyo wanga kwa woipa ndi lupanga lanu;
Zefaniya 2:12 - Buku Lopatulika Inunso Akusi, mudzaphedwa ndi lupanga langa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Inunso Akusi, mudzaphedwa ndi lupanga langa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inunso Aetiopiya, Chauta adzakukanthani ndi lupanga lake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Inunso anthu a ku Kusi, mudzaphedwa ndi lupanga.” |
Ukani Yehova, Mumtsekereze, mumgwetse, landitsani moyo wanga kwa woipa ndi lupanga lanu;
Achokera m'dziko lakutali, kumalekezero a thambo, ngakhale Yehova, ndi zida za mkwiyo wake, kuti aononge dziko lonse.
Ndipo Yehova anati, Monga mtumiki wanga Yesaya wayenda maliseche ndi wopanda nsapato zaka zitatu, akhale chizindikiro ndi chodabwitsa kwa Ejipito ndi kwa Etiopiya;
Chifukwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wako, Woyera wa Israele, Mpulumutsi wako; ndapatsa Ejipito dombolo lako, Etiopiya ndi Seba m'malo mwako.
Ndipo ndidzalimbitsa manja a mfumu ya ku Babiloni, ndi kuika lupanga langa m'dzanja lake; koma ndidzathyola manja a Farao, ndipo adzabuula pamaso pake mabuulo a munthu wopyozedwa.