Ndipo Eliya anatenga miyala khumi ndi iwiri, monga mwa ziwerengo cha mafuko ana a Yakobo, amene mau a Yehova adamfikira, kuti, Dzina lako ndi Israele.
Yoswa 4:2 - Buku Lopatulika Mudzitengere mwa anthu, amuna khumi ndi awiri, fuko limodzi mwamuna mmodzi; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mudzitengere mwa anthu, amuna khumi ndi awiri, fuko limodzi mwamuna mmodzi; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa “Sankha amuna khumi ndi aŵiri, mmodzi pa fuko lililonse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Sankha amuna khumi ndi awiri, mmodzi pa fuko lililonse. |
Ndipo Eliya anatenga miyala khumi ndi iwiri, monga mwa ziwerengo cha mafuko ana a Yakobo, amene mau a Yehova adamfikira, kuti, Dzina lako ndi Israele.
Udzitumire amuna, kuti azonde dziko la Kanani, limene ndilikupatsa ana a Israele; utumize munthu mmodzi wa fuko lililonse la makolo ao, yense kalonga pakati pa anzake.
Muwatengenso akalonga, kalonga mmodzi ku fuko limodzi, agawe dziko likhale cholowa chao.
Ndipo chinandikomera chinthu ichi; ndipo ndinatenga amuna khumi ndi awiri a inu, fuko limodzi mwamuna mmodzi;
Ndipo tsono, mudzitengere amuna khumi ndi awiri mwa mafuko a Israele, fuko limodzi mwamuna mmodzi.
ndipo muwalamulire iwo ndi kuti, Mudzitengere pano pakati pa Yordani, poimapo mapazi a ansembe, miyala khumi ndi iwiri, ndi kuoloka nayo, ndi kuiika m'mogona m'mene mugonamo usiku uno.