Yona 2:3 - Buku Lopatulika Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja, ndipo madzi anandizinga; mafunde anu onse a nyondonyondo anandimiza. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja, ndipo madzi anandizinga; mafunde anu onse a nyondonyondo anandimiza. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mudandiponya m'nyanja yozama, m'kati mwenimweni mwa njanja, ndipo mweza wam'nyanjamo udandizungulira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Munandiponya mʼnyanja yozama, mʼkati mwenimweni mwa nyanja, ndipo madzi oyenda anandizungulira; mafunde anu onse ndi mkokomo wake zinandimiza. |
Madzi akuya aitanizana ndi madzi akuya, pa mkokomo wa matiti anu; mafunde onse a nyondonyondo anandimiza ine.