koma sitidziwa uno apenyera tsopano; kapena sitimdziwa mene anamtsegulira pamaso pake; mumfunse iye; ali wamsinkhu; adzalankhula mwini za iye yekha.
Yohane 9:23 - Buku Lopatulika Chifukwa cha ichi atate wake ndi amake anati, Ali wamsinkhu; mumfunse iye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chifukwa cha ichi atate wake ndi amake anati, Ali wamsinkhu; mumfunse iye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Nchifukwa chake makolo akewo adati, “Ngwamkulu, mufunseni mwiniwakeyu.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ichi ndi chifukwa chake makolo ake anati, “Mufunseni iye ndi wamkulu.” |
koma sitidziwa uno apenyera tsopano; kapena sitimdziwa mene anamtsegulira pamaso pake; mumfunse iye; ali wamsinkhu; adzalankhula mwini za iye yekha.
Pamenepo anamuitana kachiwiri munthuyo amene anali wosaona, nati kwa iye, Lemekeza Mulungu; tidziwa kuti munthuyo ali wochimwa.