Ndipo kunali kuti anapita Iye pakati pa minda tsiku la Sabata; ndipo ophunzira ake poyenda anayamba kubudula ngala za dzinthu.
Yohane 9:14 - Buku Lopatulika Koma tsikulo ndi la Sabata limene Yesu anakanda thope, namtsegulira iye maso ake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma tsikulo ndi la Sabata limene Yesu anakanda thope, namtsegulira iye maso ake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsiku limene Yesu adaakanda thope namchiritsalo linali la Sabata. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsono linali la Sabata tsiku limene Yesu anakanda dothi ndi kutsekula maso a munthuyu. |
Ndipo kunali kuti anapita Iye pakati pa minda tsiku la Sabata; ndipo ophunzira ake poyenda anayamba kubudula ngala za dzinthu.
Ndipo panali pamene Iye analowa m'nyumba ya mmodzi wa akulu a Afarisi tsiku la Sabata, kukadya, iwo analikumzonda Iye.
Ndipo pomwepo munthuyu anachira, nayalula mphasa yake, nayenda. Koma tsiku lomwelo linali la Sabata.
Pamene ananena izi, analavula pansi, nakanda thope ndi malovuwo, napaka thopelo m'maso,