Yohane 9:12 - Buku Lopatulika Ndipo anati kwa iye, Ali kuti Iyeyo? Anena, Sindidziwa ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anati kwa iye, Ali kuti Iyeyo? Anena, Sindidziwa ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthuwo adamufunsa kuti, “Iyeyo ali kuti?” Munthu uja adati, “Kaya, sindikudziŵa.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo anamufunsa iye kuti, “Ali kuti munthu ameneyu?” Iye anati, “Ine sindikudziwa.” |
Iyeyu anayankha, Munthuyo wotchedwa Yesu anakanda thope, napaka m'maso mwanga, nati, kwa ine, Muka ku Siloamu kasambe; chifukwa chake ndinachoka, ndipo m'mene ndinasamba ndinapenya.