Pamenepo Pilato anati kwa Iye, Nanga kodi ndiwe Mfumu? Yesu anayankha, Munena kuti ndine Mfumu. Ndinabadwira ichi Ine, ndipo ndinadzera ichi kudza kudziko lapansi, kuti ndikachite umboni ndi choonadi. Yense wakukhala mwa choonadi amva mau anga.
Yohane 8:45 - Buku Lopatulika Koma Ine, chifukwa ndinena choonadi, simukhulupirira Ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Ine, chifukwa ndinena choonadi, simukhulupirira Ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Ine ndimalankhula zoona, nchifukwa chake simundikhulupirira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma chifukwa ndikuwuzani choonadi, inu simukundikhulupirira Ine! |
Pamenepo Pilato anati kwa Iye, Nanga kodi ndiwe Mfumu? Yesu anayankha, Munena kuti ndine Mfumu. Ndinabadwira ichi Ine, ndipo ndinadzera ichi kudza kudziko lapansi, kuti ndikachite umboni ndi choonadi. Yense wakukhala mwa choonadi amva mau anga.
Dziko lapansi silingathe kudana ndi inu; koma Ine lindida popeza Ine ndilichitira umboni, kuti ntchito zake zili zoipa.
Ndani mwa inu anditsutsa Ine za tchimo? Ngati ndinena choonadi, simundikhulupirira Ine chifukwa ninji?
ndi m'chinyengo chonse cha chosalungama kwa iwo akuonongeka, popeza chikondi cha choonadi sanachilandire, kuti akapulumutsidwe iwo.