Yohane 8:13 - Buku Lopatulika Chifukwa chake Afarisi anati kwa Iye, Muchita umboni wa Inu nokha; umboni wanu suli woona. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chifukwa chake Afarisi anati kwa Iye, Muchita umboni wa Inu nokha; umboni wanu suli woona. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apo Afarisi adamuuza kuti, “Ukudzichitira wekha umboni. Umboni wakowo ngwosakwanira.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Afarisi anamutsutsa Iye nati, “Iwe ukudzichitira umboni wa Iwe mwini, umboni wako siwoona.” |