Chifukwa chake imvani mau a Yehova, inu amuna amnyozo, olamulira anthu awa a mu Yerusalemu.
Yohane 7:49 - Buku Lopatulika Koma khamu ili losadziwa chilamulo, likhala lotembereredwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma khamu ili losadziwa chilamulo, likhala lotembereredwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma anthu wambaŵa sadziŵa Malamulo a Mose; ngotembereredwa basi!” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ayi! Koma gulu limene silidziwa malamulo ndi lotembereredwa.” |
Chifukwa chake imvani mau a Yehova, inu amuna amnyozo, olamulira anthu awa a mu Yerusalemu.
amene ati, Ima pa wekha, usadze chifupi ndi ine, pakuti ine ndili woyera kupambana iwe; amenewa ndiwo utsi m'mphuno mwanga, moto woyaka tsiku lonse.
Anayankha nati kwa iye, Wabadwa iwe konse m'zoipa, ndipo iwe utiphunzitse ife kodi? Ndipo anamtaya kunja.