Yohane 7:25 - Buku Lopatulika Pamenepo ena a iwo a ku Yerusalemu ananena, Kodi suyu amene afuna kumupha? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pamenepo ena a iwo a ku Yerusalemu ananena, Kodi suyu amene afuna kumupha? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo anthu ena a ku Yerusalemu adati, “Kodi munthu akufuna kumupha uja, si ameneyu? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa nthawi imeneyi anthu ena a ku Yerusalemu anayamba kufunsana kuti, “Kodi uyu si munthu uja akufuna kumuphayu? |
Ndipo taona amalankhula poyera, ndipo sanena kanthu kwa Iye. Kapena kodi akulu adziwa ndithu kuti ndiye Khristu ameneyo?