Yohane 7:21 - Buku Lopatulika Yesu anayankha nati kwa iwo, Ndinachita ntchito imodzi, ndipo muzizwa monse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Yesu anayankha nati kwa iwo, Ndinachita ntchito imodzi, ndipo muzizwa monse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adati, “Ndinangochita ntchito yozizwitsa imodzi yokha, nonsenu nkumadabwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yesu anawawuza kuti, “Ine ndinachita chodabwitsa chimodzi ndipo inu mwadabwa. |
Ngati munthu alandira mdulidwe tsiku la Sabata, kuti chilamulo cha Mose chingapasulidwe; kodi mundikwiyira Ine, chifukwa ndamchiritsadi munthu tsiku la Sabata?